Coral Sea 2800

Fomu yofunsira

Sea Recovery ndikampani yomwe imapanga makina osefa madzi mumasitima otenga athu pa nyanja zikulu zikulu. Malingana ndi ukadaulo wawo pa ntchitoyi iwowa amatha kupanga makinawa moyelekeza ndikukula kwa malo omwe mukufuna kuyikapo ndicholinga choti asamathe mmlao.

Makinawa amapezekanso mmalo omwe amayengeramo mafuta komanso sitima zonyamula katundu pa nyanja.

ZOFUNIKIRA ZOMWE ZIMAPEZEKA PA MAKINAWA   (KEY FEATURES)

Mutha kupanga ntchito yochuluka muthawi yochepa

Silikirini ya kalo yosavuta kuyitsata

Imapangidwa ndi zitsulo zopepuka (aluminium) kuti makinawa asamalemere

Amapangidwa mpchepa kuti asamathe malo muchipinda chomwe agngayikidwa

Pampu yake siyifunika kusintha oyilo

Komanso malingana ndikukonda kwanu mutha kuyikisa sefa ya otomatiki pogula

YOKHALA MBALI INA YA OTOMATIC (SEMI AUTOMATIC)

Sikilini yowonapo la LCD losavuta kugwiritsa ntchito kwake

Imadzikulisa kapena kuzichepetsa kutengera komwe madzi akuchokera pena kulumikizidwa

Imazithimitsa yokha malingana momwe inatcheredwera ikamaliza ntchito yake

 

Mita yoonetsa ndondomeko (Meter/Monitor)

Mita yotcheredwa pa ola limodzi imathandiza kuonetsetsa kuti kuti zonse zikuyenda bwino ndipo imachepesa kuonongeka kwa makinawa.Manambala a digito pa Salinity Mita amaonetsa kuchuluka kweni kweni kwa mulingo wa madzi, iziti ndi zofunika kwambiri kwa onse akugwiritsa makinawa.

Mita yotcheredwa pa ola limodzi imathandiza kutchepesa kuonongeka onongeka kwa makinawa

Mita imathandiza kuti makinawa atha kuyamba okha mmalo mondikira kuyatsidwa

Kolite yamadzi  imaonetsedwa pama sikilini 10 a LED

Mita inanso imaonetsa momwe madzi akuyendera kuperka mwayi kwa eni pampu koona zomwe zikuchitika

Mapampu (Pumps)

Mapampu opandidwa mwaukadaulo wapadera owonjezera mphavu yosefera madzi yotchedwa Booster Pump

Imabwera ndi Standard Radial Axial High Pressure Pump ndi pampu yomwe imayendera madzi basi ndipo sifuna kufewesedwa ndi oyilo kapenanso kufuna kusintha oyilo pakapita nthawi

Palinso mwayi mwayi osankha malingana ndi makondedwe:  High Pressure Plunger.

 

PAMPU IMABWERA NDI IZI (ACCESSORIES)

Sefa ya Sea Strainer yokhala pa mtetete imakhalanso ndi Monel Mesh screen yosavuta kupuputa ndiponso sefayi imateteza mibulu kuundana.

Zinthu zina ngati Commercial prefilter, Oil water separator, pH Neutralizer komanso AtuomaticFresh Flush zimabwera ndi pampuyi malingana ndikukonda kwa munthu

Zida (Materials)

Makinawa amakhala ndichida chochepesera mphavu , mawaya onse ndiotchingidwa bwino kuteteza ogwiritsa ntchito.

 Heve dute Magnetic Latching Relays (mphavu ya nyesi) yothandiza mota ikamazungulira.

Nemba yaqtsopano High Rejection /High Yield Membrane ipangitsa madzi kukhala a mtengo wapatali

Makhwala amene angapezeke madzimu amayezedwa mwapadera ndi Chemical Duty Monitor

Amabweranso ndi Fiberglass Reinforced High Pressure  Membrane  yomwe imagwiritsa  316 Stainless Steel Pressure Transducers yosachita dzimbiri ­yomwe imawerengera ndikulemba momwe makina akugwirira ntchito.

Kuteteza (Safety)

Ali ndi njira ina yomwe imatha kugawa njira ya madzi, njira imeneyi imatchedwa Product Water Diversion Valve

Makinawa amakhala ndichida chochepesera mphavu , mawaya onse ndiotchingidwa bwino kuteteza ogwiritsa ntchito.

المواصفات :

  • Zopezeka :
  • Mapangidwe : 699 gal / 442 lit per hour, 2,800 gal / 10.59 m³ per day
  • Kulemera : 980 lbs / 445 Kg