Takulandirani ku

Saeed Mohammed Al Ghandi & Sons

Kampaniyi in mu chaka cha 1972, ndipo ndi gulu limodzi la ma kampani a Al Ghandi Automotive Group imodzi ya ma kampaniotsogola  omwe amapanga makina akulu akulu a Indasitile komanso komanso zimashini  zomangira ndikupangira ntchito zosiyana siyana ku Middle East komanso ku East Africa. Mwazina ndi monga Iveco -magalimoto ochitira malonda (monga ku Dubai, Northern Emirates ndi South Sundan, Djibouti) KohlerPower Systems (Generators), MGR makina othandiza pa nkhani yosamalira zachilengedwe, Sea Recovery marine ndiponso Zoyengera madzi (Water Makers) komanso Climma Marine air conditioners.

Tipezeni motere