Aqua Matic 450-1
Aqua Matic ndimakina omwe apangidwa mwa luso ndipo ndiyosavuta kugwiritsa ntchito nkusiyana ndimakina ena omwe alipo pa msika. Makina amene angofika pa msika a Aqua Matic apangidwa ndiluso la mtengo wapatali ndipo akhonza kugwira ntchito paokha osafuna kuthandizidwa ndi munthu.