Rear-container Washer-Awa ndi makina ogwiritsa ntchito potsukira kunja ndi mkati mwa container yoyendayenda
Rear-Container Washer
-Makina otsukira kunja ndi mkati mwa ma container
-Ali ndi 6 000 litres tank yosungira madzi oyera
-5000 litres yosungira mdzi akuda
-Pump komanso makina wopopera ndikukonzera madzi akuda
-Stainless steel cleaning chamber yokhala ndi zitseko zomadzitseka zokha
-Arm grip ya mmbali ya automatic
-Sequential cleaning unit
-Hydro functions yoyendera magetsi
-Control panel mkati mwa ma monitor a woyendetsa omwe nawo amakhalanso ndi ma video camera anayi apanja
ZIDA/ ZONYAMULIRA MA BIN
-Kutsukidwa kwa mkati komanso panja pa ma container ongoyima