Side-container Washer- Iyi ndi side-container yomwe imagwiritsidwa ntchito ndi munthu mmodzi pochapira mkati komanso panja pa pa container kuyambira 1800 kufikira pa 3200 litres
SIDE-CONTAINER WASHER
-Makina ochapira kunja komanso mkati mwa ma container
-6 000 litres steel tank yosungira madzi oyera
-5000 litres tank yosungira madzi okuda, komano pump ndi makina ena omwe amachititsa kuti Thanki-yo isawonongeke
-Stainless steel cleaning chamber yomwe imakhala ndi chitseko chodzitseka chokha
-Amakhalanso ndi cleaning unit mkatikati mwa ma container
-Hydraulic system yoyendera mphamvu za magetsi
-Control panel mkati mwa ma monitor a woyendetsa yomwe ndiyolumikizana ndi ma video camera anayi apanja
ZIDA/MAKINA ONYAMULIRA MA BIN
-Ma container ochapira opezeka mkati ndi panja okhala ndi standard attachment yofikira pa 3200 litres
-Control System mkatikati mwa malo okhala woyendetsa.