MINIMACB Compactor kuchokera pa 8 kufika pa 13 m3. Nayo MINIMACB ndi Monocoque mini-compactor ya blade imodzi yomwe imakwanitsa kuchita zinthu zambiri kamba kakuti ndi ya makoni.
Kampani ya Fratelli Mazzocchia inayamba ntchito yopanga makinawa ku Frosunone mchaka cha 1967.
MUNGAYIDZIWE BWANJI MINIMACB:
-Ili ndi Labala wolimba wa silicon yemwe amachititsa kuti makinawa akhale otetezeka
-Ili ndi njira zimene zimachititsa kuti makina onyamulira ma bin adzigwira bwino ntchio
-Makina-wa amatheka kusinthidwa mmalinga ndi mmene mukufunira kuti agwilire ntchito
-Makina onyamulira ma bin omwe anyamulanso zinyalala mosavuta
-Ali ndikuthekera koyikamo chipangizo cha hydraulicturn
STANDARD EQUIPMENT
-Chipangizo chonyamulira ma bin
-Rear footboards
-Makina otsitsira katundu kuyika mu galimoto