MAZZOCCHIA SMALL SIZE COMPACTORS-JOLLY 1

Fomu yofunsira

Compactor ya Jolly1 kuchokera pa 5 kufika pa 7m3- Makina a Monocoque omwe amakhala ndi ejection blade. Makina aang`ono a Monocoque ndiwoyenera pantchito yonyamula compost,ma pepala, ma cardboard komanso kunyamula zinthu khomo ndi khomo.

Monga tawona kale mmwambamu,kampani ya Fraelli mazzocchia yakhala zaka zoposa makumi anayi ikugwira ntchitoyi ndipo kuwonjezera apo,imapanga zinthu zake malinga ndi  mmene akatswiri owona za makina osiyanasiyana pa dziko lonse amafunira

MONOCOQUE MIN-COMPACTOR YOKHALA NDI EJECTION BLADE

Rear-loading monocoque min-compactor ndiyoyenera pa ntchito yonyamulira zinthu zosiyanasiyana khomo ndi khomo.Ili ndi single-bladed compacting system.

CUSTOMIZATION

-Ili ndi ma mobile electric control pa makina onyamulira ma bin

-Stabilizer unit ya ma bin

-Ili ndi makina onyamulira matumba a zinyalala komanso onyamulira ma bin

-Makina a automatic onyamulira ma bin

-Makina ozindikiritsa komanso kuyezera kulemera

-Control panel komanso makina osungira zimene zachitika

STANDARD EQUIPMENT

-Makina onyamulira ma bin omafikira mpaka pa ma litres 1700

-Ma Rear footboards

-Chipangizo chosinthira mitundu komanso video camera

المواصفات :

  • Volume of body : 5-8 mc
  • Chassis : Two axles, light
  • MTT : From 4,5 to 8 Ton