ECO-mode yatsopano mu SK75SR imachititsa kuti izimwa mafuta ochepa pofuna kutembenuza ma SR model kuti akhale makina apamwamba kwambiri..
Kapangidwe ka makina atsopano a KOBELCO koti asamamwe mafuta kwambiri,NEXT-3E,tsopano kakugwiritsidwanso popangira zipangizo zina. ECO-mode ya mu SK75SR imamwa mafuta mochepa kwambiri ndi kutembenuza ma SR models kukhala apamwamba kwambiri. KOBELCO ikupitilira kukhala patsogolo pa ntchit yopanga ma excavator amakono.