Ndi Generator ya mphamvu ndipo idayesedwa kale bwino ndi eni ake a kampani ya KOHLER
Kampaniyi imapereka warrant ya chaka chimodzi
Electronic governor
Skid komanso Vibration Isolators
Ili ndi Line circuit breaker yayikulu
Ili ndi Radiator yabwino
Protective grille yochititsa kuti makinawa adzigwira bwino ntchito
Komanso ndi ya manual
ZOPEZEKA PA ALTERNATOR
Starter komanso charge alternator ya ma Volts 24
KAMWEDWE KA MAFUTA