KE20 ili ndi zinthu izi zomwe zimachitotsa kuti anthu ambiri idziyikonda
Kampani ya KOHLER imapereka warrant ya chaka chimodzi pa chirichonse cha pa Generator-yi
Ili ndi engine ya dizilo yomwe ili ndi charging alternator yabwino kwambiri
Ili radiator yapamwamba
Ilinso ndi thanki ya mafuta yabwino
Vibration isolators
Dry type filter
Main line breaker
Batile komanso ma cable oyambiri
CPCB- certified sound enclosure
ZOPEZEKA PA ALTERNATOR
Alternator yabwino yovomerezeka pa dziko lonse komanso ndi yamphamvu kwambiri
KAMWEDWE KA MAFUTA