KD220

Fomu yofunsira

Ma Generator  a kampani ya KOHLER Co ndi amphamvu kwambiri omwe  anayesedwa mokwanira pa kagwiridwe kake ka ntchito.

Kampaniyi imaperekanso Warrant yachaka chimodzi

Ma Generator-wa ali ndi engine ya John Deere ya mphamvu kwambiri

Ili ndi radiator yamphamvu

Ili ndi Skid komanso vibration isolators

Ili ndi Tank ya mafuta yokwana 340 litres

Ili ndi airfilter yabwino

Ili ndi circuit breaker

Ili ndi Microprocessors controller

Ili ndi ma cable, ma battery komanso batter rack

Operation ndi installation literature

ZOPEZEKA PA ALTERNATOR

KOHLER single-bearing altenator with insulation class H

100% load: 45 Lph

75% load : 34 Lph

50% load : 23 Lph

المواصفات :

  • Prime Ratings : 160 kW (200 kVA)
  • Standby Ratings : 176 kW (220 kVA)
  • Hertz : 50 Hz
  • Alternator Type : 4-pole, Rotating-Field
  • Engine Manufacturer : John Deere
  • Engine Model : 6068HFS77
  • Cylinder Arrangement : 6 Inline
  • Max Power at Rated RPM :