KT40

Fomu yofunsira

Ndiyapamwamba kwambiri komanso ili ndi ndi engine ya dizilo ya 12-volt battery charging alternator

Ili ndi radiator yomwe imafikira pa 45°C (113°F)

Thanki ya mafuta yabwino

Vibration isolators

Ili ndi airfilter yabwino

Ili ndi makina osiyanitsa mafuta ndi madzi

Ili ndi line breaker

Ili ndi battery komanso ma cable oyambira

Ili ndi ndi CPCB-certified sound enclosure

ZOPEZEKA PA ALTERNATOR

Alternator yabwino yovomerezeka pa dziko lonse komanso ndi yamphamvu kwambiri yomwe imafika pa mulingo wa BS EN 60034 komanso milingo ina yovomerezeka padziko lonse lapansi

KAMWEDWE KA MAFUTA

100% load:  9.2 Lph
75% load:  6.8 Lph
50% load:  5 Lph 

المواصفات :

  • Prime Ratings : 32 kW (40 kVA)
  • Standby Ratings :
  • Hertz : 50 Hz
  • Alternator Type : 4-pole
  • Engine Manufacturer : Tata
  • Engine Model : 497 TC
  • Cylinder Arrangement : 4 Inline
  • Max Power at Rated RPM : 47.58 kWm (63.8 BHP)