Fomu yofunsira
Ili ndi single bladed rear-loading compactor-Mac1 ndi rear-loading compactor yomwe inapangidwira kuti izigwira ntchito zolemera. Imakhala ndi container yotseka yonyamula zinyalala komanso universal rear-hinged hopper.
COMPACTOR YA SINGLE BLADE
-Monga tanenera muja, Mac1 inapangidwa kuti izigwira ntchito zolemera
-Imakhala ndi single bladed compacting system yomwe imayenda pa ma exterior tracks a pamwamba komanso komanso ma piston rods apansi amene amagwira ntchito chifukwa cha ma hydraulic cylinder anayi.
-Imataya zinyalala pogwiritsa ntchito bulkhead yamkati
-Hydraulic unit imachitidwa manage pogwiritsa ntchito magetsi
-Zipangizo zopangira ndi kutayira zinyalala zinapangidwa mogwirizana ndi malamulu a bungwe la mayiko aku Ulaya komanso mogwirizana ndi momwe zipangizo zonse za Mazzocchia zimakhalira
-Makina oyendetsera makinawa kumbala ya oyendetsa ali ndi sikilini ya tachi yomwe imaonetsa mitundu yosiyanasiyana malinga ndi mtundu wantchito yomwe ikugwiridwa.
-Ali ndi chitetezo chambiri kwa owagwiritsa ntchito.
ZIPANGIZO ZABWINO/MITUNDU YA ZONYAMULA MA BIN
-Zipangizo zonyamula ma bin zimapangidwa malinga ndi ntchito yomwe ikufuna kugwirika
-Rear footboards mothandizana ndi
-Satelite vehicles