Air Conditioners

SiteID: 9
Category: C
lnggcode: ny
id:10

AIR CONDITIONER YOKENDA NAYO YA ENVIROMAX HP

Air conditioner ya Environmax 10hp inapangidwa ngati modular heat pump.Izi zimayichititsa Air conditioner-yi kukhala yodalirika poziziritsa,kutenthetsa komanso kuchititsa zinthu kuti zikhale mmatenthedwe komanso ma ziziridwe abwino. Air conditioner-yi imagwira ntchito bwino kwambiri mma rental industry komanso mma end user application.

المواصفات :

  • Zopezeka: 208 kg
  • Kulemera: 1465 mm
  • Kutalika: 750 mm
  • Kaziziridwe: 10 kW

ENVIROMAX ENV1TW

Enviromax ENV1TW imapereka Air Conditioning yomwe ndiyoyenera ma wall installations okwera ndi otsika omwe safunikira ma ma external unit,amagwiritsa ntchito ma remote control ndi LCD display;yomwe imachititsa kuti climate control izitheka chaka chonse,compact console style yoyenerera ma dwarf walls,kuthekera kopereka mphamvu,dehumidification function built-in ndipo imapagwira ntchito bwino kwambiri.

المواصفات :

  • Zopezeka: 42 kg
  • Kulemera: 55
  • Kutalika: 93
  • Kaziziridwe: 3.2 kW

ENVIROMAX 20 AIR CONDITIONER YOYENDA NAYO

Environmax 20 inapangidwa ngati modular heat pump Air-Conditioning ndi kuthekera kwina kwa 12Kw kwa electric strip heat,kuphatikizidwa ndi heating performance ya 32Kw. Pogwiritsa ntchito cooling komanso electric resistance heating,ndipo pano imapereka dedicated dehumidification cycle.

المواصفات :

  • Zopezeka: 366 kg
  • Kulemera: 1960mm
  • Kutalika: 790mm
  • Kaziziridwe: 20 kW

CHILLER-CWS SOLO

Climma CWS SOLO,ndi system yamphamvu yomwe idapangidwira ma yatch kuti akhale ogwira ntchito bwinobwino.Imapezeka kuyambir pa 60.000 mpaka pa 144.000 BTU/h ndi compressor,reverse cycle ngati default ndipo imazima pokhapokha ikachitidwa demand,CWS SOLO ndiyoyenera pa ma yacht oyambira 55 feet kufikira pa 30 metres. MPHAMVU

المواصفات :

  • Zopezeka: 78 - 160 kg
  • Kulemera: 506 - 630 mm
  • Kutalika: 400 - 480 mm
  • Kaziziridwe: 17-35 kW

CWS DC INVERTER SERIE DC50

Climma DC Inverter chiller yatsopano idapangidwa mwamakono ndipo inapangidwa pogwiritsa ntchito upangiri omwe kampani yopanga makinawa yakhala nawo kwa zaka zoposa makumi anayi. DC chiller ya Climma imagwira ntchito chifukwa cha water cooled inverter yomwe imachepetsa mpamvu zofunikira ndi 50% kusiyana ndi ma traditional chillers.

المواصفات :

  • Zopezeka: 48 kg
  • Kulemera: 453 mm
  • Kutalika:
  • Kaziziridwe: 3 - 14 kW

CHILLER-CWS MODUL

Ma Split MK3 range apangidwira ma nautic applications ndi ma water cooled condenser,compact design,ma blowers abwino komanso a mphamvu komanso ecologic refrigerant ndipo amaperekedwa ngati standard ndi reverce cycle option

المواصفات :

  • Zopezeka: 160 - 780 kg
  • Kulemera: 653 - 704 mm
  • Kutalika: 810 - 2220 mm
  • Kaziziridwe: 21 - 253 kW

EVA SERIE FAN COIL

Ma fan coil a EVA akuwonetsa kupita patsogolo kwa kapangidwe komanso kagwiridwe ntchito ka makina kutsatira upangiri wa zaka 25 komanso luso la kapangidwe ka ma air conditioner ogwira ntchito mmadzi. Ma EVA series amenewa amachititsa kuti zinthu zambiri zokhudza system ya air-conditioning ya mmadzi zizitheka mosavuta. Kuchotsedwa kwa condensate water,blower position komanso kuthekera ndi kuchepetsedwa kwa phokoso komanso kanjenjemeredwe.

المواصفات :

  • Zopezeka: 6 - 16 kg
  • Kulemera: 219 - 308 mm
  • Kutalika: 322 - 651 mm
  • Kaziziridwe: 0.5 - 7 kW

SPLIT TYPE AC

Ma air-conditioner a Climma Split MK3 amagwira bwino ntchito pomwe pali malo ochepa,ndipo system imagawidwa mma unit awiri. Yoyamba ndi evaporator ndipo yachiwiri ndipo yachiwiri ndi compressor yomwe ikhoza kuyikidwa pogwiritsa ntchito remote.

المواصفات :

  • Zopezeka: 32- 36 kg
  • Kulemera: 291 - 304 mm
  • Kutalika: 270 - 395 mm
  • Kaziziridwe: 3 - 7 kW

COMPACT- SELF-CONTAINED AC

Ma air-conditioner a Climma Compact MK3 komanso Climma EF Independent ndiwodalirika poziziritsa ma single komanso ma adjacent cabins.Ma Compact MK3 komanso ma EF onse akonzedwa moyenerana ndi nautic application, ndi ma condenser oziziritsidwa ndi madzi,compact design,abwino komanso ma blower a mphamvu ndi ecologic refrigerant akuperekedwa ndi reverce cycle option.

المواصفات :

  • Zopezeka: 12 - 85 kg
  • Kulemera: 227 - 516 mm
  • Kutalika: 281 - 1010 mm
  • Kaziziridwe: 1 - 8 kW