Ma Excavator awa amakwaniritsa ntchito yonse yomwe ingagwiridwe ndi Excavator yayikulu. Tsopano,kwabadwa makina atsopano 80-ton ACERA GEOSPEC SK850LC omwe amagwira ntchito moyenerera.
Makina amenewa ali ndi chirichonse chomwe munthu angayembekezere kuti akhale nacho.Kamba kakagwiridwe kake ka ntchito, kapangidwe ndi maonekedwe ake, makinawa amachititsa kuti ntchito igwiridwe moyenerera OR SK75SR-3.