Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo onse iwowa anakonzanso ma SK series, excavator yatsopano yomwe inapangidwa mamakono moyenerana ndi zofuna za makampani a zomangamanga.
Atakhala pansi pofuna kupanga ma excavator a atsopano a hydraulic,a KOBELCO anaganizira zopanga makina a mphamvu zambiri kuti azigwira ntchito mosavuta koma pa nthawi yomweyo anawonetsetsanso kuti kamwedwe ka mafuta kali bwino mosapereka chiopsezo chirichonse ku zinthu zozungilira
Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo onse iwowa anakonzanso ma SK series, excavator yatsopano yomwe inapangidwa mamakono moyenerana ndi zofuna za makampani a zomangamanga