BASI YOCHEPERAPO

Fomu yofunsira

Pakadali pano Golden DragonXML6722J18 yaonjezera kutalika kwa basi yakre pokhala ndi mipando 31 ndipo ikuyendera enjini yamtundun wa 3.8L.  Basiyi tikayifananiza ndi mabsai ena omwe ali pansika kale tiona kuti iyo ikutsogola kwambiri pazichito chito zake monga, kunyamula anthu ochuluka komanso kukhala omasuka.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6722J18
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : 7245 × 2280 × 2960
  • Malo amatayala : 3935 mm
  • Mipando : 30 (27+2+1)
  • Maziziridwe a mkati : Both Front & Rear
  • Wailesi : FM/AM Radio with Mp3 Player
  • Ingini : Cummins Diesel Engine - ISF 3.8
  • Mphavu ya ingine : 105KW /2600rpm