LT7M400J-Y

Fomu yofunsira

Ma  Tower Lights a Coelmo adapangidwa kuti azitha kugwira ntchito pa malo komanso mu nyengo iliyonse. Kamba koti adapangidwa ndi zipangizo zapamwamba, ma Tower Lights a Coelmo amakhala ndi  mawalidwe ofanana ndipo amapilira mu nyengo zovuta

Ndiwodalirika mukapangidwe

Monga takamba kale, ma Tower Lights a Coelmo ndiwodalirika kamba koti mwa zina ali ndi ma stabiliser komanso adapangidwa moti akhoza kusinthidwa matalikidwe. Ma Tower a Coelmo oyima komanso oyendayenda  samasintha ngakhale akumane ndi mphepo ya mphamvu. Wolemera kapena wopepuka, amapangidwa ndi chitsulo kapena ma aluminium telescopic poles omwe amatha kukhala a manual,hydraulic kapena pneumatic extension yomwe imatha kufika mpaka pa 12 mters. Ma Tower Lights amenewa amatha kuzungulira 360°ndipo kapangidwe ka nyali zake kakhoza kuphatikizidwa ndi mitundu yosiyanasiyana ya halogen,meta halide kapena led lamps potengera ndi momwe kuwala kukufunikira.

Ma Tower Lights a Coelmo akhoza kupezeka mmalo osiyanasiyana pogwiritsa ntchito njira zosiyanasiyananso

-Ma towing trailer  oyenda pang’onopang’ono omwe ndioyenera mmalo amene mukumangidwa nyumba

-Ma towing trailer oyenda mwachangu ndi chilolezo choyenda mmisewu ikuluikulu

Standards Applied

-Control panel yokhala ndi voltmeter komanso hourmeter

-Chitetezo cha engine cha engine chomwe chimachititsa kuti engine idzizizimitsa yokha pressure ikachepa kapena engine ikatentha kwambiri

-Batile lopangidwa mommo lokhala ndi ma volts 12

-Chipangizo choyezera kachulukidwe ka mafuta

المواصفات :

  • Frequency : 50 Hz
  • A.C. Output Generator : 4x1000 W
  • Mulingo wa Thanki ya mafuta(I) : 100.00
  • Kalemeledwe(Kg) : 590